DAvideo
alle Bilder sehen ;)
Designed by: Hinx3
OSWD 2004

Valid HTML 4.01!

SELECT * FROM DAFc WHERE DAFc="UCsyv8oFopaiskbmt8sPPNoQ"

KUKHALA CHETE KWA A CHILIMA PA A CHAKWERA

🎞️ · 16.06.2024 · 08:41:48 ··· Sonntag ⭐ 147 🎬 23004 📺 Hanifa Mw
🎬 · 16.06.2024 · 08:41:48 ··· Sonntag
😎 · 03.07.2024 · 15:40:29 ··· MiTTwoch
A CHILIMA ASANKHA KUKHALA CHETE PAKULENGEZA KWA A CHAKWERA KUTI AYIMANSO
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima asankha kukhala chete pakulengeza kwa a Lazarus Chakwera amene ndi mtsogoleri wa dziko lino kuti adzayimanso pa masankho a chaka cha mawa kumachita kuti mgwirizano wawo wa Tonse umakamba kuti amene akuyenera kudzayimira pa masankhowo ndi a Chilima. Atafunisdwa lachisanu lapitali kudzera pa makina a mchezo a Whatsapp, a Chilima anangoyankha kuti palibe chimene angayankhule. Izi zikudza a Lazarus Chakwera pa 30 May 2024 atayankhula pa msonkhano wa chitukuko umene anachititsa m’boma la Lilongwe kuti adzayimira chipani cha Malawi Congress (MCP) ngati mtsogoleri wake pa masanh akubwera chaka cha mawa cha 2025.. Msonkhanowo kunali kukhazikitsa gawo lachiwiri la ntchito zachitukuko za Millennium Challenge Corporation (MCC).

· 16.06.2024 · 08:41:48 ··· Sonntag
U
U
L
L
T
* 1718520108
* 1718520108
X 23004
Y 147
P

C 20166
B 7
V 76
* · 29.07.2022 · 00:00:00 ···
2 · 09.04.2023 · 22:49:57 ···
L · 02.07.2024 · 18:44:49 ···
C · 02.07.2024 · 18:44:51 ···
💘 🖱️
* · 01.01.1970 · 01:00:00 ···
* · 01.01.1970 · 01:00:00 ···

· 01.01.1970 · 01:00:00 ···
**##
🧠 📺

*** · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::
*2* · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::
*L* · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::
*C* · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::

********