DAvideo
alle Bilder sehen ;)
Designed by: Hinx3
OSWD 2004

Valid HTML 4.01!

SELECT * FROM DAFc WHERE DAFc="UCsyv8oFopaiskbmt8sPPNoQ"

MOYO WOMVETSA CHISONI WA GEOFFREY KAPUSA MR SPLASH

🎞️ · 21.05.2024 · 21:17:17 ··· Dienstag ⭐ 66 🎬 7221 📺 Hanifa Mw
🎬 · 21.05.2024 · 21:17:17 ··· Dienstag
😎 · 03.07.2024 · 15:40:29 ··· MiTTwoch
MOYO WA GEOFFREY KAPUSA MR SPLASH
Mu chaka cha 1998, dziko la Malawi linayamba kukhala ndi television yake yoyamba imene inali ya boma. Television inatchedwa kuti Television Malawi kapena kuti TVM mwachidule ndipo inayamba ngati project imene mkulu woyambilira anasankhidwa kukhala a Benson Tembo. Ngakhale kasanjidwe kama programme komanso awulutsi ake anali ngati ongoyesera, mu gulu la anthu ogwira ntchito kumeneku kunatuluka akatswiri amene amasangalatsa anthu ndipo mmodzi mwa iwo anali a Geoffrey Kapusa amene amwalira sabata yangothayi pa 23 April 2024 pa chipatala chachikulu cha Queen Elizabeth Central Hospital mu mzinda wa Blantyre. Iwowa amasangalatsa anthu mdziko muno kudzera mu programme yawo yotchedwa Music Splash imene amayikapo kanema wa nyimbo za nthawi imeneyo. Malingana ndi mchemwali wa malemuwa, Yamikani, a Kapusa anabadwa mu chaka cha 1971 ndipo pofika chaka chino amwalira ali ndi zaka 53 zakubadwa. Kuwonjezera apo, a Kapusa amwalira ndi matenda a sugar aja amadziwika kuti diabetis pa chingerezi amene akhala akuwasautsa kwa nthawi yayitali.

· 21.05.2024 · 21:17:17 ··· Dienstag
U
U
L
L
T
* 1716319037
* 1716319037
X 7221
Y 66
P

C 20166
B 7
V 76
* · 29.07.2022 · 00:00:00 ···
2 · 09.04.2023 · 22:49:57 ···
L · 02.07.2024 · 18:44:49 ···
C · 02.07.2024 · 18:44:51 ···
💘 🖱️
* · 01.01.1970 · 01:00:00 ···
* · 01.01.1970 · 01:00:00 ···

· 01.01.1970 · 01:00:00 ···
**##
🧠 📺

*** · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::
*2* · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::
*L* · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::
*C* · 01.01.1970 · 01:00:00 ··· ::

********